1 Mbiri 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kuchokera tsiku limene ndinatulutsa Isiraeli mu Iguputo kufikira lero,+ sindinakhalepo m’nyumba, koma ndakhala m’hema ndi m’hema ndiponso m’chihema chopatulika+ ndi m’chihema chopatulika.+
5 Kuchokera tsiku limene ndinatulutsa Isiraeli mu Iguputo kufikira lero,+ sindinakhalepo m’nyumba, koma ndakhala m’hema ndi m’hema ndiponso m’chihema chopatulika+ ndi m’chihema chopatulika.+