Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 113:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Yehova wakwezeka pamwamba pa mitundu yonse ya anthu.+

      Ulemerero wake uli pamwamba pa kumwamba.+

  • Salimo 148:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Onse, anthu ndi nyama, atamande dzina la Yehova,+

      Pakuti dzina lake lokhalo lili pamwamba posafikirika.+

      Ulemerero wake uli pamwamba kuposa dziko lapansi ndi kumwamba.+

  • Yeremiya 23:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 “Kodi munthu aliyense angabisale m’malo obisika ine osamuona?”+ watero Yehova.

      “Kodi kumwamba kapena padziko lapansi, pali chilichonse chimene chingabisike kwa ine?”+ watero Yehova.

  • Machitidwe 7:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 ‘Kumwamba ndiko mpando wanga wachifumu,+ ndipo dziko lapansi ndilo chopondapo mapazi anga.+ Kodi inu mudzandimangira nyumba yotani? akutero Yehova. Kapena malo oti ine ndipumuliremo ali kuti?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena