2 Mbiri 33:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Manase anayamba kupemphera kwa Mulungu ndipo iye anamva kupembedzera kwake+ ndi pempho lake lopempha chifundo. Kenako anam’bwezera ku Yerusalemu ku ufumu wake,+ ndipo Manase anadziwa kuti Yehova ndiye Mulungu woona.+ Salimo 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova adzamva ndithu pempho langa loti andikomere mtima.+Yehova adzalandira pemphero langa.+ Salimo 119:170 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 170 Pempho langa lakuti mundichitire chifundo lifike kwa inu.+Ndipulumutseni monga mwa mawu anu.+
13 Manase anayamba kupemphera kwa Mulungu ndipo iye anamva kupembedzera kwake+ ndi pempho lake lopempha chifundo. Kenako anam’bwezera ku Yerusalemu ku ufumu wake,+ ndipo Manase anadziwa kuti Yehova ndiye Mulungu woona.+