Genesis 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Yehova anaonekera kwa Abulamu n’kumuuza kuti: “Ndidzapereka dziko ili+ kwa mbewu yako.”+ Pambuyo pake, iye anamanga pamalopo guwa lansembe la Yehova, yemwe anaonekera kwa iye. Yoswa 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Mose mtumiki wanga wamwalira.+ Tsopano konzeka limodzi ndi anthu onsewa, kuti muwoloke Yorodanoyu ndi kulowa m’dziko limene ndikulipereka kwa ana a Isiraeli.+ 2 Mbiri 6:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Muchite zimenezi n’cholinga choti iwo akuopeni,+ mwa kuyenda m’njira zanu masiku onse amene angakhale ndi moyo padziko limene munapatsa makolo athu.+
7 Ndiyeno Yehova anaonekera kwa Abulamu n’kumuuza kuti: “Ndidzapereka dziko ili+ kwa mbewu yako.”+ Pambuyo pake, iye anamanga pamalopo guwa lansembe la Yehova, yemwe anaonekera kwa iye.
2 “Mose mtumiki wanga wamwalira.+ Tsopano konzeka limodzi ndi anthu onsewa, kuti muwoloke Yorodanoyu ndi kulowa m’dziko limene ndikulipereka kwa ana a Isiraeli.+
31 Muchite zimenezi n’cholinga choti iwo akuopeni,+ mwa kuyenda m’njira zanu masiku onse amene angakhale ndi moyo padziko limene munapatsa makolo athu.+