2 Mbiri 6:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “Anthu anu akapita ku nkhondo+ kukamenyana ndi adani awo kumene inuyo mwawatumiza,+ ndipo akapemphera+ kwa inu atayang’ana kumzinda umene mwasankha ndi kunyumba ya dzina lanu imene ndamanga,+
34 “Anthu anu akapita ku nkhondo+ kukamenyana ndi adani awo kumene inuyo mwawatumiza,+ ndipo akapemphera+ kwa inu atayang’ana kumzinda umene mwasankha ndi kunyumba ya dzina lanu imene ndamanga,+