2 Mbiri 6:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 “Anthu anu akakuchimwirani+ (popeza palibe munthu amene sachimwa)+ inu n’kuwakwiyira, n’kuwapereka kwa mdani, adani awowo n’kuwagwira kupita nawo kudziko lakutali kapena lapafupi,+
36 “Anthu anu akakuchimwirani+ (popeza palibe munthu amene sachimwa)+ inu n’kuwakwiyira, n’kuwapereka kwa mdani, adani awowo n’kuwagwira kupita nawo kudziko lakutali kapena lapafupi,+