Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 6:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 inuyo mumve muli kumwamba, malo anu okhala okhazikika.+ Mumve pemphero lawo ndi pempho lawo lopempha chifundo,+ ndipo muwachitire chilungamo.+ Mukhululukire+ anthu anu amene akuchimwirani.

  • Yesaya 63:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Yang’anani muli kumwamba,+ ndipo muone kuchokera pamalo anu okhala apamwamba, oyera ndi okongola.+ Kodi mtima wanu wodzipereka kwambiri+ ndiponso mphamvu zanu zonse zili kuti? Kodi kubwadamuka kwa m’mimba mwanu+ ndi chifundo+ chanu zili kuti? Inuyo mwaleka kundichitira zimenezi.+

  • Aheberi 9:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Pakuti Khristu sanalowe m’malo oyera amkatikati opangidwa ndi manja a anthu,+ amene ndi chithunzi cha malo enieniwo,+ koma analowa kumwamba kwenikweniko.+ Tsopano ali kumwamba kuti aonekere pamaso pa Mulungu chifukwa cha ife.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena