2 Mbiri 32:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Limbani mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu.+ Musaope+ kapena kuchita mantha+ ndi mfumu ya Asuri+ ndi khamu lalikulu limene ili nalo,+ chifukwa ife tili ndi ambiri kuposa amene ali ndi mfumuyo. Salimo 46:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova wa makamu ali ndi ife.+Mulungu wa Yakobo ndiye malo athu okwezeka ndiponso achitetezo.+ [Seʹlah.]
7 “Limbani mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu.+ Musaope+ kapena kuchita mantha+ ndi mfumu ya Asuri+ ndi khamu lalikulu limene ili nalo,+ chifukwa ife tili ndi ambiri kuposa amene ali ndi mfumuyo.
7 Yehova wa makamu ali ndi ife.+Mulungu wa Yakobo ndiye malo athu okwezeka ndiponso achitetezo.+ [Seʹlah.]