Yesaya 55:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Pakuti monga momwe kumwamba kulili pamwamba kuposa dziko lapansi,+ momwemonso njira zanga n’zapamwamba kuposa njira zanu,+ ndiponso maganizo anga ndi apamwamba kuposa maganizo anu.+ Yeremiya 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ine ndikudziwa bwino, inu Yehova, kuti munthu wochokera kufumbi alibe ulamuliro wowongolera njira ya moyo wake. Munthu amene akuyenda alibe ulamuliro wowongolera mapazi ake.+
9 “Pakuti monga momwe kumwamba kulili pamwamba kuposa dziko lapansi,+ momwemonso njira zanga n’zapamwamba kuposa njira zanu,+ ndiponso maganizo anga ndi apamwamba kuposa maganizo anu.+
23 Ine ndikudziwa bwino, inu Yehova, kuti munthu wochokera kufumbi alibe ulamuliro wowongolera njira ya moyo wake. Munthu amene akuyenda alibe ulamuliro wowongolera mapazi ake.+