Deuteronomo 4:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Inuyo mwasonyezedwa zinthu zimenezi kuti mudziwe kuti Yehova ndiye Mulungu woona,+ ndipo palibenso wina.+ Yesaya 44:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Yehova, Mfumu ya Isiraeli,+ Womuwombola iye,+ Yehova wa makamu, wanena kuti: ‘Ine ndine woyamba ndi womaliza,+ ndipo palibenso Mulungu kupatulapo ine.+ Yesaya 45:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ine ndine Yehova, ndipo palibenso wina.+ Palibenso Mulungu kupatulapo ine.+ Ndidzakumanga mwamphamvu m’chiuno mwako, ngakhale kuti sukundidziwa,
35 Inuyo mwasonyezedwa zinthu zimenezi kuti mudziwe kuti Yehova ndiye Mulungu woona,+ ndipo palibenso wina.+
6 “Yehova, Mfumu ya Isiraeli,+ Womuwombola iye,+ Yehova wa makamu, wanena kuti: ‘Ine ndine woyamba ndi womaliza,+ ndipo palibenso Mulungu kupatulapo ine.+
5 Ine ndine Yehova, ndipo palibenso wina.+ Palibenso Mulungu kupatulapo ine.+ Ndidzakumanga mwamphamvu m’chiuno mwako, ngakhale kuti sukundidziwa,