2 Mbiri 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma pa tsiku la 8 anachita msonkhano wapadera+ chifukwa kwa masiku 7 anali kutsegulira guwa lansembe ndipo kwa masiku 7 ena anali kuchita chikondwerero.
9 Koma pa tsiku la 8 anachita msonkhano wapadera+ chifukwa kwa masiku 7 anali kutsegulira guwa lansembe ndipo kwa masiku 7 ena anali kuchita chikondwerero.