2 Mbiri 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho Solomo anamaliza kumanga nyumba ya Yehova+ ndi nyumba ya mfumu.+ Zilizonse zimene iye anaganiza kuchita mumtima mwake zokhudza nyumba ya Yehova ndi nyumba yake zinayenda bwino.
11 Choncho Solomo anamaliza kumanga nyumba ya Yehova+ ndi nyumba ya mfumu.+ Zilizonse zimene iye anaganiza kuchita mumtima mwake zokhudza nyumba ya Yehova ndi nyumba yake zinayenda bwino.