2 Mbiri 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo nyumba iyi ikadzakhala bwinja,+ aliyense wodutsa pafupi nayo adzayang’ana modabwa,+ ndipo ndithu adzati, ‘N’chifukwa chiyani Yehova anachita zimenezi padzikoli ndi panyumbayi?’+
21 Ndipo nyumba iyi ikadzakhala bwinja,+ aliyense wodutsa pafupi nayo adzayang’ana modabwa,+ ndipo ndithu adzati, ‘N’chifukwa chiyani Yehova anachita zimenezi padzikoli ndi panyumbayi?’+