1 Mafumu 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Solomo anatha zaka 13+ akumanga nyumba yake, ndipo anaimanga n’kuimaliza yonse.+ 2 Mbiri 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kumapeto kwa zaka 20+ zimene Solomo anamanga nyumba ya Yehova+ ndi nyumba yake,+