Yoswa 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana a Manase analephera kulanda mizindayi,+ moti Akanani anakakamira kukhalabe m’derali.+