Genesis 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pamenepo iye anati: “Ndikutemberera Kanani.+ Akhale kapolo wapansi kwambiri kwa abale ake.”+