2 Samueli 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mtumiki wanu Yowabu wachita zimenezi kuti asinthe mmene mukuonera nkhaniyi. Koma inu mbuyanga muli ndi nzeru ngati mngelo+ wa Mulungu woona, moti mukudziwa zonse za padziko lapansi.”
20 Mtumiki wanu Yowabu wachita zimenezi kuti asinthe mmene mukuonera nkhaniyi. Koma inu mbuyanga muli ndi nzeru ngati mngelo+ wa Mulungu woona, moti mukudziwa zonse za padziko lapansi.”