-
2 Mbiri 9:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 chakudya cha patebulo pake,+ mmene atumiki ake anali kukhalira pa nthawi ya chakudya, mmene atumiki ake operekera zakudya anali kuchitira, zovala zawo,+ anthu ake operekera zakumwa+ ndi zovala zawo, ndi nsembe zake zopsereza+ zimene ankapereka panyumba ya Yehova nthawi zonse,+ inazizira nkhongono ndipo inasowa chonena.
-