2 Mbiri 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 osawerengera golide wa amalonda oyendayenda,+ amalonda ena amene anali kubweretsa katundu, mafumu onse a Aluya,+ ndi abwanamkubwa a m’dzikolo amene anali kubweretsa golide ndi siliva kwa Solomo. 2 Mbiri 21:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chotero Yehova anachititsa Afilisiti+ ndi Aluya+ amene anali pafupi ndi Aitiyopiya+ kuukira Yehoramu.+
14 osawerengera golide wa amalonda oyendayenda,+ amalonda ena amene anali kubweretsa katundu, mafumu onse a Aluya,+ ndi abwanamkubwa a m’dzikolo amene anali kubweretsa golide ndi siliva kwa Solomo.
16 Chotero Yehova anachititsa Afilisiti+ ndi Aluya+ amene anali pafupi ndi Aitiyopiya+ kuukira Yehoramu.+