2 Mbiri 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pamasitepe 6 amenewo, panali zifaniziro 12 za mikango+ itaimirira, mbali iyi ndi iyi. Panalibenso ufumu wina umene unali ndi mpando wachifumu ngati umenewo.+
19 Pamasitepe 6 amenewo, panali zifaniziro 12 za mikango+ itaimirira, mbali iyi ndi iyi. Panalibenso ufumu wina umene unali ndi mpando wachifumu ngati umenewo.+