Yeremiya 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo ine ndidzapereka zigamulo zanga pa Yerusalemu ndi mizinda ya Yuda chifukwa cha zoipa zawo zonse,+ pakuti iwo andisiya ine+ ndipo amafukiza nsembe zautsi kwa milungu ina+ ndi kugwadira ntchito za manja awo.’+ Yeremiya 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ana aamuna akutola nkhuni, abambo akuyatsa moto ndipo akazi akukanda ufa kuti apange makeke okapereka nsembe kwa ‘mfumukazi yakumwamba.’+ Ndipo akuthira pansi nsembe zachakumwa+ kwa milungu ina kuti andikhumudwitse.+
16 Ndipo ine ndidzapereka zigamulo zanga pa Yerusalemu ndi mizinda ya Yuda chifukwa cha zoipa zawo zonse,+ pakuti iwo andisiya ine+ ndipo amafukiza nsembe zautsi kwa milungu ina+ ndi kugwadira ntchito za manja awo.’+
18 Ana aamuna akutola nkhuni, abambo akuyatsa moto ndipo akazi akukanda ufa kuti apange makeke okapereka nsembe kwa ‘mfumukazi yakumwamba.’+ Ndipo akuthira pansi nsembe zachakumwa+ kwa milungu ina kuti andikhumudwitse.+