1 Mafumu 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mfumuyo sinamvere anthuwo+ chifukwa zinthu zinatembenuka chonchi mwa kufuna kwa Yehova,+ kuti akwaniritse mawu amene Yehovayo analankhula+ kwa Yerobowamu mwana wa Nebati, kudzera mwa Ahiya+ Msilo. 1 Mafumu 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho Yerobowamu anauza mkazi wake kuti: “Nyamuka, udzisinthe+ kuti anthu asadziwe kuti ndiwe mkazi wa Yerobowamu ndipo upite ku Silo. Kumeneko n’kumene kuli mneneri Ahiya.+ Ameneyo ndiye anandiuza kuti ndidzakhala mfumu ya anthuwa.+ 2 Mbiri 9:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Nkhani zina zokhudza Solomo,+ zoyambirira ndi zomalizira, zinalembedwa m’mawu a mneneri Natani.+ Zalembedwanso mu ulosi wa Ahiya+ Msilo,+ ndiponso m’buku la masomphenya a Ido+ wamasomphenya, lonena za Yerobowamu+ mwana wa Nebati.+
15 Mfumuyo sinamvere anthuwo+ chifukwa zinthu zinatembenuka chonchi mwa kufuna kwa Yehova,+ kuti akwaniritse mawu amene Yehovayo analankhula+ kwa Yerobowamu mwana wa Nebati, kudzera mwa Ahiya+ Msilo.
2 Choncho Yerobowamu anauza mkazi wake kuti: “Nyamuka, udzisinthe+ kuti anthu asadziwe kuti ndiwe mkazi wa Yerobowamu ndipo upite ku Silo. Kumeneko n’kumene kuli mneneri Ahiya.+ Ameneyo ndiye anandiuza kuti ndidzakhala mfumu ya anthuwa.+
29 Nkhani zina zokhudza Solomo,+ zoyambirira ndi zomalizira, zinalembedwa m’mawu a mneneri Natani.+ Zalembedwanso mu ulosi wa Ahiya+ Msilo,+ ndiponso m’buku la masomphenya a Ido+ wamasomphenya, lonena za Yerobowamu+ mwana wa Nebati.+