Genesis 49:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Onsewa ndiwo mafuko 12 a Isiraeli, ndipo izi n’zimene bambo awo analankhula kwa iwo powadalitsa. Anapatsa aliyense wa iwo madalitso ake omuyenerera.+ Ekisodo 24:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho Mose analemba mawu onse a Yehova.+ Ndiyeno anadzuka m’mawa kwambiri n’kumanga guwa lansembe ndi zipilala 12 zoimira mafuko 12 a Isiraeli, m’tsinde mwa phiri.+
28 Onsewa ndiwo mafuko 12 a Isiraeli, ndipo izi n’zimene bambo awo analankhula kwa iwo powadalitsa. Anapatsa aliyense wa iwo madalitso ake omuyenerera.+
4 Choncho Mose analemba mawu onse a Yehova.+ Ndiyeno anadzuka m’mawa kwambiri n’kumanga guwa lansembe ndi zipilala 12 zoimira mafuko 12 a Isiraeli, m’tsinde mwa phiri.+