10 popeza Ezara anakonza+ mtima wake kuti aphunzire chilamulo cha Yehova+ ndi kuchichita+ ndiponso kuti aphunzitse+ mu Isiraeli malamulo+ ndi chilungamo.+
7 Wansembe ayenera kuphunzitsa anthu kuti adziwe Mulungu. Anthuwo ayenera kufunafuna kumva chilamulo kuchokera pakamwa pake,+ pakuti iye ndi mthenga wa Yehova wa makamu.+