1 Mafumu 12:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Yerobowamu anayamba kumanga akachisi m’malo okwezeka.+ Ndiyeno anasankha anthu wamba, anthu amene sanali ana a Levi, n’kuwaika kuti akhale ansembe.+ 1 Mafumu 13:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Pambuyo pa zimenezi, Yerobowamu sanasiyebe njira yake yoipa. Iye anapitiriza kuika anthu wamba kukhala ansembe a malo okwezeka.+ Aliyense wofuna unsembewo, iye anali kum’patsa mphamvu+ mwa kunena kuti: “Uyu akhale wansembe wa malo okwezeka.”
31 Yerobowamu anayamba kumanga akachisi m’malo okwezeka.+ Ndiyeno anasankha anthu wamba, anthu amene sanali ana a Levi, n’kuwaika kuti akhale ansembe.+
33 Pambuyo pa zimenezi, Yerobowamu sanasiyebe njira yake yoipa. Iye anapitiriza kuika anthu wamba kukhala ansembe a malo okwezeka.+ Aliyense wofuna unsembewo, iye anali kum’patsa mphamvu+ mwa kunena kuti: “Uyu akhale wansembe wa malo okwezeka.”