Salimo 95:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Bwerani timuweramire ndi kumupembedza.+Tiyeni tigwade+ pamaso pa Yehova amene ndiye Wotipanga.+ Salimo 96:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Gwadirani Yehova mutavala zovala zokongola ndi zopatulika.+Njenjemerani ndi mantha aakulu* pamaso pake, inu anthu nonse okhala padziko lapansi.+
9 Gwadirani Yehova mutavala zovala zokongola ndi zopatulika.+Njenjemerani ndi mantha aakulu* pamaso pake, inu anthu nonse okhala padziko lapansi.+