2 Mbiri 15:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma malo okwezeka+ analipobe mu Isiraeli.+ Ngakhale zinali choncho, mtima wa Asa unali wathunthu masiku ake onse.+ 2 Mbiri 20:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma sanachotse malo okwezeka+ ndiponso anthuwo anali asanakonze mitima yawo kuti atsatire Mulungu wa makolo awo.+
17 Koma malo okwezeka+ analipobe mu Isiraeli.+ Ngakhale zinali choncho, mtima wa Asa unali wathunthu masiku ake onse.+
33 Koma sanachotse malo okwezeka+ ndiponso anthuwo anali asanakonze mitima yawo kuti atsatire Mulungu wa makolo awo.+