Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 29:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Pamenepo anthu adzanena kuti, ‘N’chifukwa chakuti anataya pangano+ la Yehova Mulungu wa makolo awo, limene anapangana nawo pamene anali kuwatulutsa m’dziko la Iguputo.+

  • 2 Mafumu 17:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Iwo anapitiriza kukana malamulo ndi pangano+ limene iye anapangana ndi makolo awo, ndiponso zikumbutso+ zimene iye anali kuwachenjeza nazo. M’malomwake anayamba kutsatira mafano opanda pake+ ndipo iwowo nawonso anakhala opanda pake.+ Anatsatira mitundu imene inawazungulira, imene Yehova anawalamula kuti asamachite zofanana nayo.+

  • Nehemiya 9:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 “Koma iwo anakhala osamvera+ ndipo anakupandukirani.+ Anapitiriza kufulatira chilamulo chanu,+ ndipo anapha aneneri anu+ amene anali kuwalimbikitsa kuti abwerere kwa inu.+ Iwo anapitiriza kuchita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani.+

  • Yeremiya 34:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Anthu amene akupatuka pa pangano langa+ mwa kusatsatira mawu a m’pangano limene iwo anachita pamaso panga, ndidzawapereka kwa adani. Iwo anachita pangano limeneli mwakudula pakati+ mwana wa ng’ombe wamphongo ndi kudutsa pakati pake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena