Ekisodo 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamenepo Mose anakwera m’phirimo kukaonekera kwa Mulungu woona. Ndipo Yehova anayamba kumulankhula m’phirimo+ kuti: “Ukanene mawu awa kunyumba ya Yakobo, ana a Isiraeli kuti, Ekisodo 24:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Kwera m’phiri muno ufike kwa ine ndi kukhala momwe muno, pakuti ndikufuna kukupatsa miyala yosema imene ndalembapo chilamulo kuti ndiphunzitse anthu.”+
3 Pamenepo Mose anakwera m’phirimo kukaonekera kwa Mulungu woona. Ndipo Yehova anayamba kumulankhula m’phirimo+ kuti: “Ukanene mawu awa kunyumba ya Yakobo, ana a Isiraeli kuti,
12 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Kwera m’phiri muno ufike kwa ine ndi kukhala momwe muno, pakuti ndikufuna kukupatsa miyala yosema imene ndalembapo chilamulo kuti ndiphunzitse anthu.”+