Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 4:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Tsopano mwamuna wina wa fuko la Benjamini anathamanga kuchoka kumalo ankhondowo kukafika ku Silo tsiku limenelo, atang’amba zovala zake+ ndi kudzithira dothi kumutu.+

  • 2 Mafumu 18:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Koma Eliyakimu+ mwana wa Hilikiya amene anali woyang’anira banja lachifumu, Sebina+ mlembi, ndi Yowa+ mwana wa Asafu wolemba zochitika, anapita kwa Hezekiya atang’amba zovala zawo+ n’kumuuza mawu a Rabisake.

  • Ezara 9:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Nditangomva nkhani imeneyi, ndinang’amba zovala zanga+ n’kuyamba kuzula tsitsi la m’mutu mwanga+ ndi ndevu zanga, ndipo ndinakhala pansi ndili wokhumudwa ndi wachisoni kwambiri.+

  • Yobu 1:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Yobu atamva zimenezi anaimirira n’kung’amba+ malaya ake akunja odula manja. Anametanso tsitsi+ kumutu kwake, kenako anagwada pansi+ n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena