Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Maliro 1:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Yehova wandichotsera anthu anga onse amphamvu+ ndi kuwakankhira pambali.

      Wandiitanitsira msonkhano kuti athyolethyole anyamata anga.+

      Yehova wapondaponda moponderamo mphesa+ mwa namwali, mwana wamkazi wa Yuda.+

  • Maliro 2:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kodi ndikusonyeze umboni wotani? Kodi ndingakuyerekezere ndi chiyani, iwe mwana wamkazi wa Yerusalemu?+

      Kodi ndikufananitse ndi chiyani kuti ndikutonthoze, namwali iwe, mwana wamkazi wa Ziyoni?+

      Pakuti kuwonongeka+ kwako kwafalikira ngati kukula kwa nyanja. Ndani angakuchiritse?+

  • Mika 4:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Koma iwe nsanja ya gulu la nkhosa, malo okwera a mwana wamkazi wa Ziyoni,+ ulamuliro udzabwerera kwa iwe. Ulamuliro woyamba, ufumu wa mwana wamkazi wa Yerusalemu,+ udzabwerera kwa iwe.+

  • Zekariya 9:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Iwe mwana wamkazi wa Ziyoni sangalala kwambiri.+ Fuula mokondwera+ iwe mwana wamkazi wa Yerusalemu. Taona, mfumu yako+ ikubwera kwa iwe.+ Mfumuyo ndi yolungama ndipo yapambana.+ Iyo ndi yodzichepetsa+ ndipo ikubwera itakwera bulu. Ikubwera itakwera nyama yokhwima, imene ndi mwana wamphongo wa bulu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena