Yobu 22:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Olungama adzaona chiwonongeko chawo n’kusangalala,+Ndipo wosalakwa adzawaseka kuti: