Yesaya 37:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ukakhala phee, ukamatuluka,+ ndiponso ukamalowa, ine ndimadziwa bwino,+Ndimadziwanso ukandipsera mtima,+
28 Ukakhala phee, ukamatuluka,+ ndiponso ukamalowa, ine ndimadziwa bwino,+Ndimadziwanso ukandipsera mtima,+