Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 32:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Anthu inu, musakhale ngati hatchi kapena nyulu* yosazindikira,+

      Imene munthu amachita kuimanga chingwe chapakamwa ndi chapamutu kuti athetse kupulupudza kwake,+

      Ndi kuti aiyandikire.”+

  • Ezekieli 38:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndithu ine ndidzakubweza n’kukukola chibwano ndi ngowe.+ Kenako ndidzakukokera pafupi limodzi ndi gulu lako lonse lankhondo,+ mahatchi ako ndi asilikali ako okwera pamahatchi. Asilikali onsewa ndi ovala mwaulemerero.+ Iwo ndi khamu lalikulu lonyamula zishango zazikulu ndi zazing’ono, ndipo onsewo ndi aluso lomenya nkhondo pogwiritsa ntchito malupanga.+

  • Amosi 4:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, walumbira mwa kuyera kwake+ kuti, ‘“Taonani! Masiku adzafika pamene mudzanyamulidwa ndi ngowe zokolera nyama ndipo otsala anu adzawakola ndi mbedza za nsomba.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena