2 Mafumu 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pa nthawiyi, Hezekiya anafunsa Yesaya kuti: “Kodi chizindikiro chakuti Yehova andichiritsa, ndi kuti ndidzapitadi kunyumba ya Yehova pa tsiku lachitatu n’chiyani?”+ Salimo 65:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo anthu okhala m’madera akutali adzachita mantha ndi zizindikiro zanu,+Mudzachititsa kulowa ndi kutuluka kwa dzuwa kufuula mokondwera.+ Yesaya 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Pempha chizindikiro kwa Yehova Mulungu wako.+ Chikhoza kukhala chozama ngati Manda kapena chachitali ngati malo okwera.”
8 Pa nthawiyi, Hezekiya anafunsa Yesaya kuti: “Kodi chizindikiro chakuti Yehova andichiritsa, ndi kuti ndidzapitadi kunyumba ya Yehova pa tsiku lachitatu n’chiyani?”+
8 Ndipo anthu okhala m’madera akutali adzachita mantha ndi zizindikiro zanu,+Mudzachititsa kulowa ndi kutuluka kwa dzuwa kufuula mokondwera.+
11 “Pempha chizindikiro kwa Yehova Mulungu wako.+ Chikhoza kukhala chozama ngati Manda kapena chachitali ngati malo okwera.”