Yoswa 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mana analeka kugwa pa tsikuli, pamene ana a Isiraeli anadya zokolola za m’dzikomo. Kuyambira pamenepo, mana sanagwenso pakati pa ana a Isiraeli.+ Chotero, chaka chimenechi n’chimene iwo anayamba kudya zokolola za m’dziko la Kanani.+ 1 Mafumu 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ufa umene uli mumtsuko waukulu siutha, ndipo mafuta amene ali mumtsuko waung’ono saatha, kufikira tsiku limene Yehova adzagwetse mvula padziko lapansi.’”+ Yohane 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu onsewo atakhuta,+ iye anauza ophunzira ake kuti: “Sonkhanitsani zotsala zonse, kuti pasawonongeke chilichonse.”
12 Mana analeka kugwa pa tsikuli, pamene ana a Isiraeli anadya zokolola za m’dzikomo. Kuyambira pamenepo, mana sanagwenso pakati pa ana a Isiraeli.+ Chotero, chaka chimenechi n’chimene iwo anayamba kudya zokolola za m’dziko la Kanani.+
14 Pakuti Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ufa umene uli mumtsuko waukulu siutha, ndipo mafuta amene ali mumtsuko waung’ono saatha, kufikira tsiku limene Yehova adzagwetse mvula padziko lapansi.’”+
12 Anthu onsewo atakhuta,+ iye anauza ophunzira ake kuti: “Sonkhanitsani zotsala zonse, kuti pasawonongeke chilichonse.”