2 Mbiri 34:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako anapereka ndalamazo m’manja mwa ogwira ntchito osankhidwa a m’nyumba ya Yehova.+ Ndiyeno iwowa anapereka ndalamazo kwa anthu amene anali kugwira ntchito m’nyumba ya Yehova, omwe anazigwiritsa ntchito yokonzera nyumbayo.
10 Kenako anapereka ndalamazo m’manja mwa ogwira ntchito osankhidwa a m’nyumba ya Yehova.+ Ndiyeno iwowa anapereka ndalamazo kwa anthu amene anali kugwira ntchito m’nyumba ya Yehova, omwe anazigwiritsa ntchito yokonzera nyumbayo.