2 Mafumu 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Amuna amene ankapatsidwa ndalama kuti azipereke kwa anthu ogwira ntchito,+ sankafunsidwa+ mmene ayendetsera ndalamazo chifukwa ankagwira ntchito mokhulupirika.+
15 Amuna amene ankapatsidwa ndalama kuti azipereke kwa anthu ogwira ntchito,+ sankafunsidwa+ mmene ayendetsera ndalamazo chifukwa ankagwira ntchito mokhulupirika.+