Yobu 34:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti iye amapereka mphoto kwa munthu wochokera kufumbi malinga ndi zochita zake,+Ndipo amam’bweretsera zinthu zogwirizana ndi njira yake. Yeremiya 23:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mneneri amene walota maloto anene maloto akewo. Koma amene ndamuuza mawu anga, alankhule mawu angawo moona.”+ “Kodi mapesi a tirigu angafanane ndi tirigu weniweniyo?”+ watero Yehova.
11 Pakuti iye amapereka mphoto kwa munthu wochokera kufumbi malinga ndi zochita zake,+Ndipo amam’bweretsera zinthu zogwirizana ndi njira yake.
28 Mneneri amene walota maloto anene maloto akewo. Koma amene ndamuuza mawu anga, alankhule mawu angawo moona.”+ “Kodi mapesi a tirigu angafanane ndi tirigu weniweniyo?”+ watero Yehova.