Yoswa 24:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pa tsikulo, Yoswa anachita pangano ndi anthuwo ndi kuwaikira lamulo ndi chigamulo+ ku Sekemu. 2 Mbiri 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kuwonjezera apo, anachita pangano+ loti adzafunafuna Yehova Mulungu wa makolo awo ndi mtima wawo wonse ndi moyo wawo wonse.+ 2 Mbiri 23:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako Yehoyada anachita pangano pakati pa iyeyo, anthu onse, ndi mfumu kuti anthuwo apitiriza kukhala anthu+ a Yehova.
12 Kuwonjezera apo, anachita pangano+ loti adzafunafuna Yehova Mulungu wa makolo awo ndi mtima wawo wonse ndi moyo wawo wonse.+
16 Kenako Yehoyada anachita pangano pakati pa iyeyo, anthu onse, ndi mfumu kuti anthuwo apitiriza kukhala anthu+ a Yehova.