Ezekieli 44:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Koma Alevi amene anachoka kwa ine n’kupita kutali+ adzakumana ndi zotsatira za zochita zawo. Iwo anachoka kwa ine pamene Aisiraeli anandisiya n’kutsatira mafano awo onyansa.+ Malaki 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Koma inu mwapatuka panjira yoyenera.+ Mwalepheretsa anthu ambiri kutsatira chilamulo.+ Mwaphwanya pangano limene ndinapangana ndi Levi,”+ watero Yehova wa makamu.
10 “‘Koma Alevi amene anachoka kwa ine n’kupita kutali+ adzakumana ndi zotsatira za zochita zawo. Iwo anachoka kwa ine pamene Aisiraeli anandisiya n’kutsatira mafano awo onyansa.+
8 “Koma inu mwapatuka panjira yoyenera.+ Mwalepheretsa anthu ambiri kutsatira chilamulo.+ Mwaphwanya pangano limene ndinapangana ndi Levi,”+ watero Yehova wa makamu.