1 Mafumu 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Nkhani zina zokhudza Rehobowamu ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’nthawi ya mafumu a Yuda. 2 Mafumu 21:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Nkhani zina zokhudza Manase ndi zonse zimene anachita, ndiponso tchimo lake limene anachita, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Yuda.
29 Nkhani zina zokhudza Rehobowamu ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’nthawi ya mafumu a Yuda.
17 Nkhani zina zokhudza Manase ndi zonse zimene anachita, ndiponso tchimo lake limene anachita, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Yuda.