1 Mafumu 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mfumu Solomo inaitana anthu ogwira ntchito yokakamiza+ kuti adzamange nyumba ya Yehova,+ nyumba yake, Chimulu cha Dothi,*+ khoma+ lozungulira Yerusalemu, ndiponso mizinda ya Hazori,+ Megido,+ ndi Gezeri.+ Zekariya 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pa tsiku limenelo, anthu adzalira kwambiri mu Yerusalemu ngati mmene analirira ku Hadadirimoni, m’chigwa cha Megido.+
15 Mfumu Solomo inaitana anthu ogwira ntchito yokakamiza+ kuti adzamange nyumba ya Yehova,+ nyumba yake, Chimulu cha Dothi,*+ khoma+ lozungulira Yerusalemu, ndiponso mizinda ya Hazori,+ Megido,+ ndi Gezeri.+
11 Pa tsiku limenelo, anthu adzalira kwambiri mu Yerusalemu ngati mmene analirira ku Hadadirimoni, m’chigwa cha Megido.+