2 Mbiri 28:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 M’mizinda yonse ya Yuda anamangamo malo okwezeka+ operekera nsembe zautsi kwa milungu ina.+ Chotero anakwiyitsa+ Yehova Mulungu wa makolo ake. 2 Mbiri 33:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anamanga maguwa ansembe+ m’nyumba ya Yehova, imene ponena za iyo Yehova anati: “Dzina langa lidzakhala ku Yerusalemu mpaka kalekale.”+
25 M’mizinda yonse ya Yuda anamangamo malo okwezeka+ operekera nsembe zautsi kwa milungu ina.+ Chotero anakwiyitsa+ Yehova Mulungu wa makolo ake.
4 Anamanga maguwa ansembe+ m’nyumba ya Yehova, imene ponena za iyo Yehova anati: “Dzina langa lidzakhala ku Yerusalemu mpaka kalekale.”+