2 Mafumu 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano Elisa anauza mayi amene anamuukitsira mwana uja,+ kuti: “Nyamuka, iwe ndi banja lako, ukakhale monga mlendo kulikonse kumene ungakakhale,+ chifukwa Yehova abweretsa njala.+ Njalayo idzatenga zaka 7.”+
8 Tsopano Elisa anauza mayi amene anamuukitsira mwana uja,+ kuti: “Nyamuka, iwe ndi banja lako, ukakhale monga mlendo kulikonse kumene ungakakhale,+ chifukwa Yehova abweretsa njala.+ Njalayo idzatenga zaka 7.”+