2 Mafumu 23:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Yehoahazi anali ndi zaka 23+ pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira miyezi itatu ku Yerusalemu. Mayi ake anali a ku Libina, ndipo dzina lawo linali Hamutali+ mwana wa Yeremiya.
31 Yehoahazi anali ndi zaka 23+ pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira miyezi itatu ku Yerusalemu. Mayi ake anali a ku Libina, ndipo dzina lawo linali Hamutali+ mwana wa Yeremiya.