1 Mafumu 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Solomo anatha zaka 13+ akumanga nyumba yake, ndipo anaimanga n’kuimaliza yonse.+ Amosi 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndidzatumiza moto mu Yuda ndipo udzanyeketsa nsanja zokhalamo za Yerusalemu.’+