Yesaya 49:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kodi mayi angaiwale mwana wake woyamwa, osamvera chisoni mwana wochokera m’mimba mwake?+ Ngakhale amayi amenewa akhoza kuiwala,+ koma ine sindidzakuiwala.+ Yesaya 66:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mofanana ndi munthu amene mayi ake amamutonthoza, inenso ndidzakutonthozani anthu inu,+ ndipo mudzatonthozedwa chifukwa cha Yerusalemu.+
15 Kodi mayi angaiwale mwana wake woyamwa, osamvera chisoni mwana wochokera m’mimba mwake?+ Ngakhale amayi amenewa akhoza kuiwala,+ koma ine sindidzakuiwala.+
13 Mofanana ndi munthu amene mayi ake amamutonthoza, inenso ndidzakutonthozani anthu inu,+ ndipo mudzatonthozedwa chifukwa cha Yerusalemu.+