1 Mafumu 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pambuyo pa zimenezi, mwana wamwamuna wa mayi wa m’nyumbamo, anadwala. Matenda ake anakula kwambiri mpaka anamwalira.+ Mlaliki 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti munthu+ nayenso sadziwa nthawi yake.+ Monga nsomba zimene zagwidwa mu ukonde wakupha,+ ndi mbalame zimene zakodwa mumsampha,+ ana a anthu nawonso amakodwa pa nthawi yatsoka,+ nthawiyo ikawafikira mwadzidzidzi.+
17 Pambuyo pa zimenezi, mwana wamwamuna wa mayi wa m’nyumbamo, anadwala. Matenda ake anakula kwambiri mpaka anamwalira.+
12 Pakuti munthu+ nayenso sadziwa nthawi yake.+ Monga nsomba zimene zagwidwa mu ukonde wakupha,+ ndi mbalame zimene zakodwa mumsampha,+ ana a anthu nawonso amakodwa pa nthawi yatsoka,+ nthawiyo ikawafikira mwadzidzidzi.+