-
Yeremiya 52:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Mumzindawo anatengamo nduna imodzi ya panyumba ya mfumu imene inali kuyang’anira amuna ankhondo. Anatenganso amuna 7 kuchokera pa anthu amene ankatha kuonana ndi mfumu mwa amuna amene anali mumzindamo.+ Komanso anatenga mlembi wa mkulu wa asilikali yemwe anali kusonkhanitsa ankhondo a m’dzikolo, ndi amuna 60 mwa anthu a m’dzikolo amene anali mumzindawo.+
-